Beschreibung
Produktdetails
Format
ePUB
Kopierschutz
Ja
Family Sharing
Ja
Text-to-Speech
Ja
Erscheinungsdatum
20.12.2025
Verlag
Dag Heward-MillsSeitenzahl
(Printausgabe)
Dateigröße
338 KB
Sprache
Englisch
EAN
9798896064947
Yesu anagwiritsa ntchito mawu akuti "kulira ndi kukukuta mano" maulendo asanu osiyana m'Baibulo. Ndi chenjezo la uneneri lonena za ululu, mkwiyo, chisoni, kunong'oneza bondo, chikumbumtima, ndi malingaliro a kutayika omwe adzamvedwe pa kulowa kumwamba opanda kukhala wokonzekera uko. Wolemba mabuku wotchuka, Dag Heward-Mills m'njira yake yachizolowezi yosakayikitsa, akufotokoza chowonadi chochititsa mantha cha anthu angati amene adzanong'oneze bondo chifukwa cha kutaya mwayi ali padziko lapansi. Inu muyenera kuchita chilichonse chimene mungathe kuti mupewe kukhala m'gulu la anthu amene adzalira ndi kukukuta mano awo m'kunong'oneza bondo!
Noch keine Bewertungen vorhanden
Verfassen Sie die erste Bewertung zu diesem Artikel
Helfen Sie anderen Kundinnen und Kunden durch Ihre Meinung.